Ezekieli 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndikukhuthulira mkwiyo wanga posachedwapa,+ ndipo ndisonyeza mkwiyo wanga wonse pa iwe.+ Ndidzakuweruza mogwirizana ndi njira zako ndiponso kukulanga chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene umachita.
8 Ndikukhuthulira mkwiyo wanga posachedwapa,+ ndipo ndisonyeza mkwiyo wanga wonse pa iwe.+ Ndidzakuweruza mogwirizana ndi njira zako ndiponso kukulanga chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene umachita.