Ezekieli 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ndinachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina kumene ankakhalako.+ Chifukwa ndinachititsa kuti iwo* andidziwe pamaso pa anthu a mitundu inawo pamene ndinawatulutsa* mʼdziko la Iguputo.+
9 Koma ndinachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina kumene ankakhalako.+ Chifukwa ndinachititsa kuti iwo* andidziwe pamaso pa anthu a mitundu inawo pamene ndinawatulutsa* mʼdziko la Iguputo.+