Ezekieli 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa iwe muli munthu amene amachita zonyansa ndi mkazi wa mnzake.+ Wina amadetsa mpongozi wake wamkazi pochita naye khalidwe lonyansa+ ndipo wina amagona ndi mchemwali wake, mwana wamkazi wa bambo ake enieni.+
11 Mwa iwe muli munthu amene amachita zonyansa ndi mkazi wa mnzake.+ Wina amadetsa mpongozi wake wamkazi pochita naye khalidwe lonyansa+ ndipo wina amagona ndi mchemwali wake, mwana wamkazi wa bambo ake enieni.+