Ezekieli 36:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mukadzachita zimenezi mudzakhala mʼdziko limene ndinapatsa makolo anu. Mudzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.’+
28 Mukadzachita zimenezi mudzakhala mʼdziko limene ndinapatsa makolo anu. Mudzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.’+