Ezekieli 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzawachititsa kuti akhale mtundu umodzi mʼdzikolo+ ndipo azidzakhala mʼmapiri a Isiraeli. Onse azidzalamulidwa ndi mfumu imodzi+ ndipo sadzakhalanso mitundu iwiri kapena kugawanika nʼkukhala maufumu awiri.+
22 Ndidzawachititsa kuti akhale mtundu umodzi mʼdzikolo+ ndipo azidzakhala mʼmapiri a Isiraeli. Onse azidzalamulidwa ndi mfumu imodzi+ ndipo sadzakhalanso mitundu iwiri kapena kugawanika nʼkukhala maufumu awiri.+