Ezekieli 44:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 ‘Ndipo cholowa chawo ndi ichi: Cholowa chawo ndi ine.+ Musawapatse malo alionse mu Isiraeli, chifukwa cholowa chawo ndi ine. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:28 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, tsa. 15
28 ‘Ndipo cholowa chawo ndi ichi: Cholowa chawo ndi ine.+ Musawapatse malo alionse mu Isiraeli, chifukwa cholowa chawo ndi ine.