-
Ezekieli 47:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Mugawane dzikoli kuti likhale cholowa chanu ndi cha alendo omwe akukhala pakati panu, amene abereka ana pa nthawi imene amakhala nanu. Kwa inu, alendowo akhale ngati nzika za Isiraeli. Iwo alandire cholowa pamodzi ndi inu pakati pa mafuko a Isiraeli.
-