Danieli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mfumuyo inayankha Akasidiwo kuti: “Ndikukuuzani komaliza kuti: Ngati simundiuza zimene ndalota nʼkundimasulira, ndikudulani nthulinthuli ndipo nyumba zanu ndidzazisandutsa zimbudzi za anthu onse.*
5 Mfumuyo inayankha Akasidiwo kuti: “Ndikukuuzani komaliza kuti: Ngati simundiuza zimene ndalota nʼkundimasulira, ndikudulani nthulinthuli ndipo nyumba zanu ndidzazisandutsa zimbudzi za anthu onse.*