Danieli 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mtengowo ndi inuyo mfumu, chifukwa mwakula ndipo mwakhala wamphamvu. Ulemerero wanu wakula mpaka kukafika kumwamba+ ndipo ulamuliro wanu wafika kumalekezero a dziko lapansi.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:22 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32 Ulosi wa Danieli, ptsa. 86-87
22 Mtengowo ndi inuyo mfumu, chifukwa mwakula ndipo mwakhala wamphamvu. Ulemerero wanu wakula mpaka kukafika kumwamba+ ndipo ulamuliro wanu wafika kumalekezero a dziko lapansi.+