-
Danieli 4:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndiyeno inu mfumu munaona mlonda,+ mthenga woyera akutsika kuchokera kumwamba, ndipo ankanena kuti: “Gwetsani mtengowo ndipo muuwononge, koma musiye chitsa ndi mizu yake munthaka ndipo muchikulunge ndi mkombero wachitsulo ndi wakopa.* Chitsacho chikhale pakati pa udzu wakutchire ndipo chizinyowa ndi mame akumwamba. Chizikhala limodzi ndi nyama zakutchire mpaka patadutsa nthawi zokwana 7.”+
-