Danieli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ambiri adzadzitsuka, adzadziyeretsa ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa, koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:10 Ulosi wa Danieli, ptsa. 296-297, 300
10 Anthu ambiri adzadzitsuka, adzadziyeretsa ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa, koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+