15 Kuyambira nthawi imeneyo kupita mʼtsogolo ndidzamubwezera minda yake ya mpesa.+
Ndidzamupatsanso chigwa cha Akori+ kuti chikhale ngati khomo lachiyembekezo.
Kumeneko adzayankha ngati mmene ankayankhira ali mtsikana,
Ngatinso pa tsiku limene anatuluka mʼdziko la Iguputo.’+