Hoseya 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe Samariya, fano lako la mwana wa ngʼombe lakanidwa.+ Ndakwiyira kwambiri anthu ako.+ Kodi iwo adzalephera kukhala osalakwa mpaka liti?
5 Iwe Samariya, fano lako la mwana wa ngʼombe lakanidwa.+ Ndakwiyira kwambiri anthu ako.+ Kodi iwo adzalephera kukhala osalakwa mpaka liti?