Hoseya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Efuraimu adzamudula ngati mtengo.+ Muzu wake udzauma ndipo sadzaberekanso zipatso. Komanso ngati angabereke ana, ndidzapha ana ake okondedwawo.”
16 Efuraimu adzamudula ngati mtengo.+ Muzu wake udzauma ndipo sadzaberekanso zipatso. Komanso ngati angabereke ana, ndidzapha ana ake okondedwawo.”