Hoseya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu a ku Samariya adzachita mantha ndi fano la mwana wa ngʼombe la ku Beti-aveni.+ Anthu ake adzalilirira.Nawonso ansembe a mulungu wachilendo, amene ankasangalala ndi fanolo komanso ulemerero wake, adzalilirira.Chifukwa lidzatengedwa kupita kudziko lina. Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:5 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, tsa. 179/1/1998, ptsa. 22-233/1/1989, tsa. 14
5 Anthu a ku Samariya adzachita mantha ndi fano la mwana wa ngʼombe la ku Beti-aveni.+ Anthu ake adzalilirira.Nawonso ansembe a mulungu wachilendo, amene ankasangalala ndi fanolo komanso ulemerero wake, adzalilirira.Chifukwa lidzatengedwa kupita kudziko lina.