Yoweli 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Lengezani kwa anthu a mitundu ina+ kuti: ‘Konzekerani nkhondo! Konzekeretsani amuna amphamvu! Asilikali onse abwere nʼkuukira!+ Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Tsiku la Yehova, ptsa. 168-169 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 22-235/1/1992, ptsa. 8-9
9 Lengezani kwa anthu a mitundu ina+ kuti: ‘Konzekerani nkhondo! Konzekeretsani amuna amphamvu! Asilikali onse abwere nʼkuukira!+