Amosi 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wanena kuti,‘Popeza Isiraeli anandigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa chakuti anagulitsa munthu wolungama kuti apeze siliva,Komanso munthu wosauka kuti apeze nsapato.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, ptsa. 17-18
6 Yehova wanena kuti,‘Popeza Isiraeli anandigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa chakuti anagulitsa munthu wolungama kuti apeze siliva,Komanso munthu wosauka kuti apeze nsapato.+