Amosi 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Funafunani Yehova kuti mupitirize kukhala ndi moyo.+Kuti asakuyakireni ngati moto panyumba ya Yosefe.Nʼkuwotcheratu Beteli popanda wozimitsa motowo. Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,11/2017, tsa. 2
6 Funafunani Yehova kuti mupitirize kukhala ndi moyo.+Kuti asakuyakireni ngati moto panyumba ya Yosefe.Nʼkuwotcheratu Beteli popanda wozimitsa motowo.