Amosi 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa ndikudziwa kuchuluka kwa zochita zanu zondigalukira,Ndiponso kukula kwa machimo anu.Mumachitira nkhanza munthu wolungama,Mumalandira ziphuphu,Komanso mumaphwanya ufulu wa anthu osauka pageti la mzinda.+
12 Chifukwa ndikudziwa kuchuluka kwa zochita zanu zondigalukira,Ndiponso kukula kwa machimo anu.Mumachitira nkhanza munthu wolungama,Mumalandira ziphuphu,Komanso mumaphwanya ufulu wa anthu osauka pageti la mzinda.+