Mika 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsoka kwa ine, chifukwa ndili ngati munthu amene,Nthawi yokolola zipatso zamʼchilimwe* itatha,Komanso nthawi yokunkha mʼmunda umene akololamo mphesa itatha,Sanapeze mphesa zoti adye.Komanso nkhuyu zoyambirira zimene akulakalaka.
7 Tsoka kwa ine, chifukwa ndili ngati munthu amene,Nthawi yokolola zipatso zamʼchilimwe* itatha,Komanso nthawi yokunkha mʼmunda umene akololamo mphesa itatha,Sanapeze mphesa zoti adye.Komanso nkhuyu zoyambirira zimene akulakalaka.