Zefaniya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ndamva kunyoza kwa Mowabu+ ndi mawu achipongwe a Aamoni,+Amene ankanenera anthu anga nʼkumadzitama kuti alanda dziko lawo.”+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, tsa. 203/1/1996, ptsa. 11-12, 14
8 “Ndamva kunyoza kwa Mowabu+ ndi mawu achipongwe a Aamoni,+Amene ankanenera anthu anga nʼkumadzitama kuti alanda dziko lawo.”+