Zefaniya 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno ndinati, ‘Mosakayikira udzandiopa ndipo udzalola kulangizidwa,’+ Kuti iye* asawonongedwe.+Ndidzamuimba mlandu wa zonsezi.* Koma mʼpamene ankafunitsitsa kwambiri kuchita zoipa.+
7 Ndiyeno ndinati, ‘Mosakayikira udzandiopa ndipo udzalola kulangizidwa,’+ Kuti iye* asawonongedwe.+Ndidzamuimba mlandu wa zonsezi.* Koma mʼpamene ankafunitsitsa kwambiri kuchita zoipa.+