Zekariya 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo anthu amumzinda wina adzapita kwa anthu amumzinda wina nʼkuwauza kuti: “Tiyeni tipite tikapemphe Yehova kuti atikomere mtima* komanso tikafunefune Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Inenso ndipita nawo.”+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:21 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, ptsa. 21-224/15/1986, tsa. 17
21 Ndipo anthu amumzinda wina adzapita kwa anthu amumzinda wina nʼkuwauza kuti: “Tiyeni tipite tikapemphe Yehova kuti atikomere mtima* komanso tikafunefune Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Inenso ndipita nawo.”+