Zekariya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ndinatenga ndodo yanga yotchedwa Wosangalatsa+ ija nʼkuiduladula. Ndinachita izi kuti ndithetse pangano limene ndinachita ndi anthu a mtundu wanga. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:10 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, tsa. 31
10 Choncho ndinatenga ndodo yanga yotchedwa Wosangalatsa+ ija nʼkuiduladula. Ndinachita izi kuti ndithetse pangano limene ndinachita ndi anthu a mtundu wanga.