Mateyu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako panafika munthu wakhate. Munthuyo anamugwadira nʼkunena kuti: “Ambuye, ndikudziwa kuti ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+
2 Kenako panafika munthu wakhate. Munthuyo anamugwadira nʼkunena kuti: “Ambuye, ndikudziwa kuti ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+