Mateyu 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yesu anatambasula dzanja lake nʼkumukhudza ndipo ananena kuti: “Inde ndikufuna. Khala woyera.”+ Nthawi yomweyo khate lakelo linatha.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Yesu—Ndi Njira, tsa. 65 Nsanja ya Olonda,12/1/2008, tsa. 54/15/1986, tsa. 8-9
3 Choncho Yesu anatambasula dzanja lake nʼkumukhudza ndipo ananena kuti: “Inde ndikufuna. Khala woyera.”+ Nthawi yomweyo khate lakelo linatha.+