Mateyu 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwenso Kaperenao,+ kodi mwina udzakwezedwa kumwamba? Ayi, koma udzatsikira ku Manda,*+ chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Sodomu, mzindawo ukanakhala ulipobe mpaka lero. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:23 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 16-176/1/1988, tsa. 301/15/1987, tsa. 24-25 Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 179
23 Iwenso Kaperenao,+ kodi mwina udzakwezedwa kumwamba? Ayi, koma udzatsikira ku Manda,*+ chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Sodomu, mzindawo ukanakhala ulipobe mpaka lero.
11:23 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 16-176/1/1988, tsa. 301/15/1987, tsa. 24-25 Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 179