Maliko 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero Yesu anamuyankha kuti: “Ndithu ndikukuuza iwe kuti lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:30 Nsanja ya Olonda,8/1/1991, tsa. 22
30 Atatero Yesu anamuyankha kuti: “Ndithu ndikukuuza iwe kuti lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+