Maliko 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwamsanga mʼbandakucha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu komanso alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi kuti agwirizane zoti amuchite Yesu. Kenako anamumanga nʼkupita naye kukamupereka kwa Pilato.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 290 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 30-31 Nsanja ya Olonda,12/1/1990, tsa. 8
15 Mwamsanga mʼbandakucha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu komanso alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi kuti agwirizane zoti amuchite Yesu. Kenako anamumanga nʼkupita naye kukamupereka kwa Pilato.+