Luka 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno mu Yerusalemu munali munthu wina dzina lake Simiyoni. Mwamuna ameneyu anali wolungama komanso wodzipereka kwa Mulungu. Iye ankayembekezera nthawi imene Mulungu adzatonthoze Isiraeli+ ndipo mzimu woyera unali pa iye. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:25 Nsanja ya Olonda,3/15/1994, tsa. 24
25 Ndiyeno mu Yerusalemu munali munthu wina dzina lake Simiyoni. Mwamuna ameneyu anali wolungama komanso wodzipereka kwa Mulungu. Iye ankayembekezera nthawi imene Mulungu adzatonthoze Isiraeli+ ndipo mzimu woyera unali pa iye.