Luka 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zimenezi zitachitika, Yesu anachokako. Kenako anaona munthu wina wokhometsa msonkho dzina lake Levi atakhala mu ofesi yokhomeramo msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:27 Yesu—Ndi Njira, tsa. 68 Nsanja ya Olonda,5/15/1986, tsa. 8
27 Zimenezi zitachitika, Yesu anachokako. Kenako anaona munthu wina wokhometsa msonkho dzina lake Levi atakhala mu ofesi yokhomeramo msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.”+