-
Luka 13:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Komanso, anthu adzabwera kuchokera kumʼmawa, kumadzulo, kumpoto ndi kumʼmwera ndipo adzakhala patebulo mu Ufumu wa Mulungu.
-