-
Luka 24:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Iwo anayamba kuuzana kuti: “Kodi si paja tinakhudzidwa kwambiri mumtima pamene amalankhula nafe mumsewu muja ndi kutifotokozera Malemba momveka bwino?”
-