Yohane 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Atate wako ali kuti?” Yesu anayankha kuti: “Inu simukundidziwa komanso simukudziwa Atate wanga.+ Mukanandidziwa ine, mukanadziwanso Atate wanga.”+
19 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Atate wako ali kuti?” Yesu anayankha kuti: “Inu simukundidziwa komanso simukudziwa Atate wanga.+ Mukanandidziwa ine, mukanadziwanso Atate wanga.”+