Yohane 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yesu anayankha kuti: “Kodi masana sali ndi maola 12?+ Munthu akamayenda masana palibe chimamupunthwitsa, chifukwa amaona kuwala kwa dzikoli. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:9 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 210-211 Nsanja ya Olonda,4/15/1989, tsa. 24
9 Yesu anayankha kuti: “Kodi masana sali ndi maola 12?+ Munthu akamayenda masana palibe chimamupunthwitsa, chifukwa amaona kuwala kwa dzikoli.