Yohane 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno gulu la anthulo linamuyankha kuti: “Ife tinamva mʼChilamulo kuti Khristu adzakhala kosatha.+ Nanga inu mukunena bwanji kuti Mwana wa munthu ayenera kukwezedwa mʼmwamba?+ Kodi Mwana wa munthu ameneyo ndi ndani?” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:34 Yesu—Ndi Njira, tsa. 242 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, tsa. 8
34 Ndiyeno gulu la anthulo linamuyankha kuti: “Ife tinamva mʼChilamulo kuti Khristu adzakhala kosatha.+ Nanga inu mukunena bwanji kuti Mwana wa munthu ayenera kukwezedwa mʼmwamba?+ Kodi Mwana wa munthu ameneyo ndi ndani?”