-
Yohane 19:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiye Pilato atamva mawu amenewa, anatulutsa Yesu panja, ndipo iye anakhala pampando woweruzira milandu, pamalo amene ankatchulidwa kuti Bwalo Lamiyala, koma pa Chiheberi ankatchulidwa kuti Gabʹba·tha.
-