Machitidwe 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu aliyense amene sadzamvera Mneneriyo, Mulungu adzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu.’+