-
Machitidwe 12:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mngeloyo anamuuza kuti: “Vala zovala zako ndi nsapato zako.” Iye anachitadi zimenezo. Kenako anamuuza kuti: “Vala malaya ako akunja ndipo uzinditsatira.”
-