-
Machitidwe 12:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma atazindikira mawu a Petulo, anasangalala kwambiri moti mʼmalo motsegula getilo, anathamangira mkati nʼkukanena kuti Petulo ali pageti.
-