Machitidwe 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwamuna ameneyu anaphunzitsidwa* njira ya Yehova.* Iye anali wodzipereka kwambiri chifukwa chakuti anali ndi mzimu woyera, ndipo ankalankhula ndi kuphunzitsa molondola za Yesu. Koma ankangodziwa za ubatizo wa Yohane wokha. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:25 Nsanja ya Olonda,6/15/2010, tsa. 1110/1/1996, ptsa. 20-21
25 Mwamuna ameneyu anaphunzitsidwa* njira ya Yehova.* Iye anali wodzipereka kwambiri chifukwa chakuti anali ndi mzimu woyera, ndipo ankalankhula ndi kuphunzitsa molondola za Yesu. Koma ankangodziwa za ubatizo wa Yohane wokha.