28 Iwo ankafuula kuti: “Inu Aisiraeli, tithandizeni! Munthu uyu akuphunzitsa zotsutsana ndi anthu a mtundu wathu kulikonse. Iyeyu akuphunzitsanso zotsutsana ndi Chilamulo komanso malo ano. Kuwonjezera pamenepo, watenga Agiriki nʼkuwalowetsa mʼkachisi ndipo waipitsa malo oyerawa.”+