Aroma 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kukhala Myuda weniweni kuli mumtima+ ndipo mdulidwe wake umakhalanso wamumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo amatamandidwa ndi Mulungu, osati anthu.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:29 Nsanja ya Olonda,6/15/2003, tsa. 142/1/1998, tsa. 16
29 Kukhala Myuda weniweni kuli mumtima+ ndipo mdulidwe wake umakhalanso wamumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo amatamandidwa ndi Mulungu, osati anthu.+