Aroma 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa kuganizira kwambiri zinthu za thupi kumayambitsa udani ndi Mulungu+ popeza thupi siligonjera lamulo la Mulungu, ndipotu kunena zoona, silingaligonjere. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:7 Nsanja ya Olonda,3/1/1991, tsa. 2112/1/1990, tsa. 30
7 Chifukwa kuganizira kwambiri zinthu za thupi kumayambitsa udani ndi Mulungu+ popeza thupi siligonjera lamulo la Mulungu, ndipotu kunena zoona, silingaligonjere.