-
Aroma 16:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Chifukwa anthu oterowo si akapolo a Ambuye wathu Khristu, koma a mimba zawo. Ndipo amagwiritsa ntchito mawu okopa ndiponso achinyengo kuti apusitse anthu oona mtima.
-