1 Akorinto 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ayi, koma ndikutanthauza kuti zinthu zimene anthu a mitundu ina amapereka nsembe amazipereka kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+ Ndipo sindikufuna kuti muzichita chilichonse chogwirizana ndi ziwanda.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:20 Nsanja ya Olonda,2/15/2004, tsa. 51/15/1993, ptsa. 22-2412/1/1990, tsa. 5
20 Ayi, koma ndikutanthauza kuti zinthu zimene anthu a mitundu ina amapereka nsembe amazipereka kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+ Ndipo sindikufuna kuti muzichita chilichonse chogwirizana ndi ziwanda.+