2 Akorinto 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithudi inuyo munaona umboni wakuti ndine mtumwi. Munaona kuti ndinapirira kwambiri,+ ndinachita zizindikiro, zinthu zodabwitsa ndiponso ntchito zamphamvu.+
12 Ndithudi inuyo munaona umboni wakuti ndine mtumwi. Munaona kuti ndinapirira kwambiri,+ ndinachita zizindikiro, zinthu zodabwitsa ndiponso ntchito zamphamvu.+