Aefeso 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inde, pa nthawi ina pamene tinkakhala pakati pawo, tinkachita zinthu motsatira zilakolako za thupi lathu.+ Tinkachita zofuna za thupi ndi maganizo athu,+ ndipo mwachibadwa tinali ana oyenera kulandira mkwiyo wa Mulungu+ mofanana ndi ena onse. Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:3 Nsanja ya Olonda,9/1/1995, tsa. 44/15/1987, tsa. 10-11 Kukambitsirana, tsa. 360
3 Inde, pa nthawi ina pamene tinkakhala pakati pawo, tinkachita zinthu motsatira zilakolako za thupi lathu.+ Tinkachita zofuna za thupi ndi maganizo athu,+ ndipo mwachibadwa tinali ana oyenera kulandira mkwiyo wa Mulungu+ mofanana ndi ena onse.