Aefeso 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mogwirizana ndi iye, inunso limodzi ndi anthu ena mukumangidwa pamodzi kuti mukhale malo oti Mulungu akhalemo mwa mzimu.+
22 Mogwirizana ndi iye, inunso limodzi ndi anthu ena mukumangidwa pamodzi kuti mukhale malo oti Mulungu akhalemo mwa mzimu.+