Aefeso 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anachita zimenezi kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero, wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zoterezi,+ koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:27 Nsanja ya Olonda,6/1/2008, ptsa. 13-14
27 Anachita zimenezi kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero, wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zoterezi,+ koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+